2 Atesalonika 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Amenewa adzawaweruza kuti alandire chilango+ cha chiwonongeko chamuyaya,+ kuwachotsa pamaso pa Ambuye ndi ku ulemerero wa mphamvu zake.+ Chivumbulutso 6:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iwo anali kuuza mapiri ndi matanthwe mosalekeza kuti: “Tigwereni,+ tibiseni kuti tisaonekere kwa Iye amene wakhala pampando wachifumu,+ ndiponso kuti tibisike ku mkwiyo wa Mwanawankhosa,+
9 Amenewa adzawaweruza kuti alandire chilango+ cha chiwonongeko chamuyaya,+ kuwachotsa pamaso pa Ambuye ndi ku ulemerero wa mphamvu zake.+
16 Iwo anali kuuza mapiri ndi matanthwe mosalekeza kuti: “Tigwereni,+ tibiseni kuti tisaonekere kwa Iye amene wakhala pampando wachifumu,+ ndiponso kuti tibisike ku mkwiyo wa Mwanawankhosa,+