Salimo 18:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pa nthawi ya zowawa zanga ndinaitana Yehova,Ndinafuulira Mulungu wanga kuti andithandize.+Iye anamva mawu anga ali m’kachisi wake.+Pamenepo makutu ake anamva kulira kwanga kopempha thandizo.+ Salimo 66:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndithudi, Mulungu wamva,+Wamvetsera mwatcheru mawu a pemphero langa.+
6 Pa nthawi ya zowawa zanga ndinaitana Yehova,Ndinafuulira Mulungu wanga kuti andithandize.+Iye anamva mawu anga ali m’kachisi wake.+Pamenepo makutu ake anamva kulira kwanga kopempha thandizo.+