Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 66:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pakuti inu Mulungu mwatisanthula,+

      Mwatiyenga ngati siliva.+

  • Salimo 94:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Wodala ndi munthu wamphamvu amene inu Ya mumamudzudzula,+

      Komanso amene inu mumamuphunzitsa chilamulo chanu,+

  • Yesaya 53:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Koma zinamukomera Yehova kuti mtumiki wake aphwanyidwe.+ Iye anamulola kuti adwale.+ Mukapereka moyo wake monga nsembe ya kupalamula,+ iye adzaona ana ake.+ Adzatalikitsa masiku ake+ ndipo ndi dzanja lake, adzakwaniritsa zokonda+ Yehova.+

  • 2 Akorinto 6:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 ngati osadziwika koma odziwika bwino,+ ngati oti tikufa koma tikukhalabe ndi moyo,+ ngati olangidwa+ koma osakaphedwa,+

  • Aheberi 12:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Pakuti Yehova amalanga aliyense amene iye amamukonda, ndipo amakwapula aliyense amene iye amamulandira monga mwana wake.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena