Salimo 19:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Malamulo+ ochokera kwa Yehova ndi olungama,+ amasangalatsa mtima.+Chilamulo+ cha Yehova ndi choyera,+ chimatsegula maso.+ Salimo 119:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Taonani! Ine ndikulakalaka malamulo anu.+Ndisungeni wamoyo mogwirizana ndi chilungamo chanu.+ Miyambo 30:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mawu alionse a Mulungu ndi oyera.+ Iye ndi chishango kwa onse othawira kwa iye.+
8 Malamulo+ ochokera kwa Yehova ndi olungama,+ amasangalatsa mtima.+Chilamulo+ cha Yehova ndi choyera,+ chimatsegula maso.+