2 Mafumu 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kenako anamuuza kuti: “Tiye tipitire limodzi ukaone kuti sindilekerera zoti anthu azipikisana+ ndi Yehova.” Chotero Yehonadabu anapita limodzi ndi anthuwo atakwera m’galeta lankhondo la Yehu. Salimo 69:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti kudzipereka kwambiri panyumba yanu kwandidya,+Ndipo mnyozo wa anthu amene akukutonzani wagwa pa ine.+ Yohane 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pamenepo ophunzira ake anakumbukira zimene Malemba amanena, kuti amati: “Kudzipereka kwambiri panyumba yanu kudzandidya.”+
16 Kenako anamuuza kuti: “Tiye tipitire limodzi ukaone kuti sindilekerera zoti anthu azipikisana+ ndi Yehova.” Chotero Yehonadabu anapita limodzi ndi anthuwo atakwera m’galeta lankhondo la Yehu.
9 Pakuti kudzipereka kwambiri panyumba yanu kwandidya,+Ndipo mnyozo wa anthu amene akukutonzani wagwa pa ine.+
17 Pamenepo ophunzira ake anakumbukira zimene Malemba amanena, kuti amati: “Kudzipereka kwambiri panyumba yanu kudzandidya.”+