1 Mbiri 22:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yehova akupatse nzeru ndi kuzindikira.+ Akupatsenso lamulo lotsogolera Isiraeli, kuti usunge chilamulo cha Yehova Mulungu wako.+ 2 Mbiri 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mundipatse nzeru ndi luntha lodziwa zinthu+ kuti ndizitha kutsogolera+ anthuwa, pakuti ndani angaweruze anthu anu ochulukawa?”+ Miyambo 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 komanso ukaitana kumvetsa zinthu+ ndi kufuulira kuzindikira,+ Yakobo 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Choncho ngati wina akusowa nzeru,+ azipempha kwa Mulungu,+ ndipo adzamupatsa,+ popeza iye amapereka mowolowa manja kwa onse ndiponso amapereka mosatonza.+
12 Yehova akupatse nzeru ndi kuzindikira.+ Akupatsenso lamulo lotsogolera Isiraeli, kuti usunge chilamulo cha Yehova Mulungu wako.+
10 Mundipatse nzeru ndi luntha lodziwa zinthu+ kuti ndizitha kutsogolera+ anthuwa, pakuti ndani angaweruze anthu anu ochulukawa?”+
5 Choncho ngati wina akusowa nzeru,+ azipempha kwa Mulungu,+ ndipo adzamupatsa,+ popeza iye amapereka mowolowa manja kwa onse ndiponso amapereka mosatonza.+