Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 8:40
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 40 Muchite zimenezi n’cholinga choti iwo akuopeni,+ masiku onse amene angakhale ndi moyo padziko limene munapatsa makolo athu.+

  • Salimo 2:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Tumikirani Yehova mwamantha.+

      Kondwerani ndipo nthunthumirani.+

  • Yeremiya 33:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Mzindawu udzakhala ndi dzina limene lidzandikondweretsa,+ dzina lochititsa kuti nditamandidwe ndi kulandira ulemerero pakati pa mitundu yonse ya padziko lapansi imene idzamva za zinthu zabwino zimene ndikuwachitira.+ Anthu a mitundu inawo adzachita mantha+ ndi kunjenjemera+ chifukwa cha zinthu zabwino ndi mtendere wonse umene ndikubweretsa pamzindawu.’”+

  • Machitidwe 9:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Pamenepo mpingo+ mu Yudeya monse, mu Galileya, ndi mu Samariya unalowa m’nyengo yamtendere, ndipo unakhala wolimba. Popeza kuti unali kuyenda moopa Yehova+ ndiponso kulimbikitsidwa ndi mzimu woyera,+ mpingowo unali kukulirakulira.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena