Nehemiya 6:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndiyeno adani athu onse atangomva zimenezi,+ komanso anthu a mitundu ina yotizungulira ataona, anachita manyazi ndipo anadziwa kuti ntchito imeneyi yatheka chifukwa cha Mulungu wathu.+
16 Ndiyeno adani athu onse atangomva zimenezi,+ komanso anthu a mitundu ina yotizungulira ataona, anachita manyazi ndipo anadziwa kuti ntchito imeneyi yatheka chifukwa cha Mulungu wathu.+