Salimo 29:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 M’patseni Yehova ulemerero woyenera dzina lake.+Weramirani Yehova mutavala zovala zopatulika zokongola.+ Salimo 148:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Onse, anthu ndi nyama, atamande dzina la Yehova,+Pakuti dzina lake lokhalo lili pamwamba posafikirika.+Ulemerero wake uli pamwamba kuposa dziko lapansi ndi kumwamba.+
2 M’patseni Yehova ulemerero woyenera dzina lake.+Weramirani Yehova mutavala zovala zopatulika zokongola.+
13 Onse, anthu ndi nyama, atamande dzina la Yehova,+Pakuti dzina lake lokhalo lili pamwamba posafikirika.+Ulemerero wake uli pamwamba kuposa dziko lapansi ndi kumwamba.+