Yesaya 55:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Pakuti monga momwe kumwamba kulili pamwamba kuposa dziko lapansi,+ momwemonso njira zanga n’zapamwamba kuposa njira zanu,+ ndiponso maganizo anga ndi apamwamba kuposa maganizo anu.+
9 “Pakuti monga momwe kumwamba kulili pamwamba kuposa dziko lapansi,+ momwemonso njira zanga n’zapamwamba kuposa njira zanu,+ ndiponso maganizo anga ndi apamwamba kuposa maganizo anu.+