Salimo 7:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inu Yehova Mulungu wanga, ngati ndachita cholakwa chilichonse,+Ngati manja anga achita zosalungama zilizonse,+ Salimo 17:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mwasanthula mtima wanga, mwandifufuza usiku,+Ndipo mwandiyenga. Mudzaona kuti sindinaganizire kuchita choipa chilichonse.+Pakamwa panga sipadzaphwanya malamulo.+
3 Inu Yehova Mulungu wanga, ngati ndachita cholakwa chilichonse,+Ngati manja anga achita zosalungama zilizonse,+ Salimo 17:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mwasanthula mtima wanga, mwandifufuza usiku,+Ndipo mwandiyenga. Mudzaona kuti sindinaganizire kuchita choipa chilichonse.+Pakamwa panga sipadzaphwanya malamulo.+
3 Mwasanthula mtima wanga, mwandifufuza usiku,+Ndipo mwandiyenga. Mudzaona kuti sindinaganizire kuchita choipa chilichonse.+Pakamwa panga sipadzaphwanya malamulo.+