Salimo 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Inu Yehova Mulungu wanga,+ ine ndathawira kwa inu.+Ndipulumutseni kwa onse ondizunza ndipo mundilanditse,+ Salimo 35:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Amene akufunafuna moyo wanga achite manyazi ndi kunyozeka.+Amene akundikonzera chiwembu muwabweze ndipo athedwe nzeru.+
7 Inu Yehova Mulungu wanga,+ ine ndathawira kwa inu.+Ndipulumutseni kwa onse ondizunza ndipo mundilanditse,+ Salimo 35:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Amene akufunafuna moyo wanga achite manyazi ndi kunyozeka.+Amene akundikonzera chiwembu muwabweze ndipo athedwe nzeru.+
4 Amene akufunafuna moyo wanga achite manyazi ndi kunyozeka.+Amene akundikonzera chiwembu muwabweze ndipo athedwe nzeru.+