Genesis 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Pa chiyambi,+ Mulungu+ analenga+ kumwamba ndi dziko lapansi.+ Genesis 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mulungu tsopano anati: “Pakhale mlengalenga+ pakati pa madzi, ndiponso pakhale cholekanitsa pakati pa madzi ndi madzi.”+ Salimo 33:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kumwamba kunalengedwa ndi mawu a Yehova,+Ndipo makamu ake onse analengedwa ndi mpweya wa m’kamwa mwake.+
6 Mulungu tsopano anati: “Pakhale mlengalenga+ pakati pa madzi, ndiponso pakhale cholekanitsa pakati pa madzi ndi madzi.”+
6 Kumwamba kunalengedwa ndi mawu a Yehova,+Ndipo makamu ake onse analengedwa ndi mpweya wa m’kamwa mwake.+