Salimo 55:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 Inu Mulungu, mvetserani pemphero langa.+Musanyalanyaze pempho langa lakuti mundikomere mtima.+ Salimo 65:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Inu Wakumva pemphero, anthu a mitundu yonse adzabwera kwa inu.+ 1 Petulo 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pakuti maso+ a Yehova* ali pa olungama, ndipo makutu ake amamva pembedzero lawo,+ koma nkhope ya Yehova imakwiyira anthu ochita zoipa.”+
12 Pakuti maso+ a Yehova* ali pa olungama, ndipo makutu ake amamva pembedzero lawo,+ koma nkhope ya Yehova imakwiyira anthu ochita zoipa.”+