Salimo 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mvetserani mawu anga+ inu Yehova,Mumvetse kudandaula kwanga. Salimo 80:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 80 Inu M’busa wa Isiraeli, tcherani khutu,+Inu amene mukutsogolera Yosefe ngati gulu la nkhosa.+Inu amene mwakhala pa akerubi,+ walani.+ Salimo 84:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova Mulungu wa makamu, imvani pemphero langa,+Tcherani khutu, inu Mulungu wa Yakobo.+ [Seʹlah.] 1 Petulo 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pakuti maso+ a Yehova* ali pa olungama, ndipo makutu ake amamva pembedzero lawo,+ koma nkhope ya Yehova imakwiyira anthu ochita zoipa.”+
80 Inu M’busa wa Isiraeli, tcherani khutu,+Inu amene mukutsogolera Yosefe ngati gulu la nkhosa.+Inu amene mwakhala pa akerubi,+ walani.+
12 Pakuti maso+ a Yehova* ali pa olungama, ndipo makutu ake amamva pembedzero lawo,+ koma nkhope ya Yehova imakwiyira anthu ochita zoipa.”+