Miyambo 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pita kwa nyerere+ waulesi iwe,+ ukaone mmene imachitira zinthu kuti ukhale wanzeru. Miyambo 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Waulesi amalakalaka zinthu, chonsecho moyo wake ulibe chilichonse.+ Koma anthu akhama adzanenepa.+ Miyambo 19:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Munthu waulesi amapisa dzanja lake m’mbale yodyera,+ koma n’kulephera kulibweretsa pakamwa.+