Yoswa 23:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Koma mukatembenuka+ n’kumamatira zotsala za anthu awa a mitundu ina,+ amene atsala pakati panuwa, kumakwatirana nawo,+ n’kumakhala pakati pawo, iwonso n’kumakhala pakati panu, Yoswa 23:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 dziwani kuti Yehova Mulungu wanu adzaleka kuwapitikitsa pamaso panu.+ Iwo adzakhala ngati msampha ndiponso ngati khwekhwe kwa inu.+ Adzakhalanso ngati zokubayani* m’mbali mwanu komanso ngati zitsotso m’maso mwanu, kufikira mutatheratu padziko labwinoli limene Yehova Mulungu wanu wakupatsani.+ Salimo 11:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye adzavumbitsira oipa misampha, moto ndi sulufule,+Komanso mphepo yotentha, monga gawo limene ayenera kumwa.+
12 “Koma mukatembenuka+ n’kumamatira zotsala za anthu awa a mitundu ina,+ amene atsala pakati panuwa, kumakwatirana nawo,+ n’kumakhala pakati pawo, iwonso n’kumakhala pakati panu,
13 dziwani kuti Yehova Mulungu wanu adzaleka kuwapitikitsa pamaso panu.+ Iwo adzakhala ngati msampha ndiponso ngati khwekhwe kwa inu.+ Adzakhalanso ngati zokubayani* m’mbali mwanu komanso ngati zitsotso m’maso mwanu, kufikira mutatheratu padziko labwinoli limene Yehova Mulungu wanu wakupatsani.+
6 Iye adzavumbitsira oipa misampha, moto ndi sulufule,+Komanso mphepo yotentha, monga gawo limene ayenera kumwa.+