Salimo 37:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Ona munthu wosalakwa ndipo yang’anitsitsa munthu wolungama,+Pakuti tsogolo la munthu ameneyu ndi lamtendere.+ Yeremiya 29:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “‘Maganizo anga kwa inu ndikuwadziwa bwino. Ndikuganizira+ zokupatsani mtendere osati masoka,+ kuti mukhale ndi chiyembekezo chabwino ndiponso tsogolo labwino,’+ watero Yehova. Aroma 6:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma tsopano chifukwa munamasulidwa ku uchimo ndipo munakhala akapolo a Mulungu,+ mukukhala ndi zipatso+ za chiyero, ndipo pa mapeto pake mudzakhala ndi moyo wosatha.+
37 Ona munthu wosalakwa ndipo yang’anitsitsa munthu wolungama,+Pakuti tsogolo la munthu ameneyu ndi lamtendere.+
11 “‘Maganizo anga kwa inu ndikuwadziwa bwino. Ndikuganizira+ zokupatsani mtendere osati masoka,+ kuti mukhale ndi chiyembekezo chabwino ndiponso tsogolo labwino,’+ watero Yehova.
22 Koma tsopano chifukwa munamasulidwa ku uchimo ndipo munakhala akapolo a Mulungu,+ mukukhala ndi zipatso+ za chiyero, ndipo pa mapeto pake mudzakhala ndi moyo wosatha.+