Salimo 19:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 N’zolakalakika kuposa golide, kuposa golide wambiri woyengeka bwino.+N’zotsekemera* kuposa uchi,+ inde kuposa uchi umene ukukha m’zisa.+ Salimo 119:103 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 103 Mawu anu amatsekemera m’kamwa mwanga,Kuposa mmene uchi umakomera!+ Miyambo 22:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pakuti n’chinthu chosangalatsa kuti uzisunge mumtima mwako,+ kuti zikhazikike pamilomo yako.+
10 N’zolakalakika kuposa golide, kuposa golide wambiri woyengeka bwino.+N’zotsekemera* kuposa uchi,+ inde kuposa uchi umene ukukha m’zisa.+