Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 31:50
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 50 Tsopano lolani kuti aliyense wa ife apereke zimene wabwera nazo monga chopereka kwa Yehova,+ zinthu zagolide, matcheni ovala m’miyendo, zibangili, mphete zachifumu,+ ndolo,* ndi zodzikongoletsera zina za akazi.+ Tipereke zimenezi kwa Yehova kuti ziphimbe machimo athu.”

  • Deuteronomo 16:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 “Mwamuna aliyense pakati panu azikaonekera katatu pa chaka pamaso pa Yehova Mulungu wanu, pamalo amene Mulungu adzasankhe.+ Azikaonekera pa chikondwerero cha mkate wopanda chofufumitsa,+ chikondwerero cha masabata+ ndi pa chikondwerero cha misasa.+ Palibe amene ayenera kuonekera kwa Yehova chimanjamanja.+

  • Luka 16:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 “Nanunso ndikukuuzani kuti, Dzipezereni mabwenzi+ ndi chuma chosalungama,+ kuti chumacho chikatha, akakulandireni m’malo okhala amuyaya.+

  • 1 Timoteyo 6:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Uwalamule kuti azichita zabwino,+ akhale olemera pa ntchito zabwino,+ owolowa manja, okonzeka kugawira ena,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena