Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 39:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Mbuye wakeyo anaona kuti Yehova anali ndi mnyamatayo, ndi kuti chilichonse chimene anali kuchita, Yehova anali kuchidalitsa.

  • Miyambo 10:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Wogwira ntchito ndi dzanja laulesi adzakhala wosauka,+ koma dzanja la munthu wakhama ndi limene limalemeretsa.+

  • Miyambo 12:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Ulesi sungavumbulutse nyama zimene munthu akufuna kusaka,+ koma munthu wakhama ndiye chuma chamtengo wapatali cha munthu.

  • Akolose 3:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Chilichonse chimene mukuchita, muzichichita ndi moyo wanu wonse+ ngati kuti mukuchitira Yehova,+ osati anthu,

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena