Salimo 72:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Padziko lapansi padzakhala tirigu wambiri.+Pamwamba pa mapiri padzakhala tirigu wochuluka.+Zokolola za mfumu zidzachuluka ngati mitengo ya ku Lebanoni,+Ndipo anthu ochokera mumzinda adzaphuka ngati udzu wa panthaka.+ Salimo 104:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Amameretsa msipu kuti nyama zidye,+Ndipo amameretsa mbewu kuti anthu agwiritse ntchito.+Amachita zimenezi kuti chakudya chituluke m’nthaka,+
16 Padziko lapansi padzakhala tirigu wambiri.+Pamwamba pa mapiri padzakhala tirigu wochuluka.+Zokolola za mfumu zidzachuluka ngati mitengo ya ku Lebanoni,+Ndipo anthu ochokera mumzinda adzaphuka ngati udzu wa panthaka.+
14 Amameretsa msipu kuti nyama zidye,+Ndipo amameretsa mbewu kuti anthu agwiritse ntchito.+Amachita zimenezi kuti chakudya chituluke m’nthaka,+