Miyambo 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Munthu adzatamandidwa chifukwa cha pakamwa pake panzeru,+ koma wa mtima wopotoka adzanyozedwa.+