1 Samueli 25:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho mudziwe zimenezi ndi kuona zimene mungachite, chifukwa atsimikiza kudzetsa tsoka+ pa mbuyanga ndi onse a m’nyumba yake, pakuti mbuye wathu ndi munthu wopanda pake,+ sitingathe kulankhula naye.” Mateyu 27:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye anati: “Ndachimwa popereka munthu wolungama.”*+ Koma iwo anamuyankha kuti: “Ife sizikutikhudza zimenezo. Udziwa wekha chochita!”+ Machitidwe 12:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Nthawi yomweyo mngelo wa Yehova anamukantha,+ chifukwa sanapereke ulemerero kwa Mulungu.+ Ndipo anadyedwa ndi mphutsi n’kumwalira.
17 Choncho mudziwe zimenezi ndi kuona zimene mungachite, chifukwa atsimikiza kudzetsa tsoka+ pa mbuyanga ndi onse a m’nyumba yake, pakuti mbuye wathu ndi munthu wopanda pake,+ sitingathe kulankhula naye.”
4 Iye anati: “Ndachimwa popereka munthu wolungama.”*+ Koma iwo anamuyankha kuti: “Ife sizikutikhudza zimenezo. Udziwa wekha chochita!”+
23 Nthawi yomweyo mngelo wa Yehova anamukantha,+ chifukwa sanapereke ulemerero kwa Mulungu.+ Ndipo anadyedwa ndi mphutsi n’kumwalira.