Esitere 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Zimenezi zitachitika, Moredekai anabwerera kuchipata cha mfumu.+ Koma Hamani anapita kunyumba kwake mofulumira, akulira ndiponso ataphimba kumutu.+ Salimo 132:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Adani ake ndidzawaveka manyazi,+Koma ufumu*+ wake udzapita patsogolo.”+ Miyambo 26:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chikwapu n’cha hatchi,+ zingwe n’za pakamwa pa bulu,+ ndipo ndodo ndi yokwapulira msana wa anthu opusa.+
12 Zimenezi zitachitika, Moredekai anabwerera kuchipata cha mfumu.+ Koma Hamani anapita kunyumba kwake mofulumira, akulira ndiponso ataphimba kumutu.+
3 Chikwapu n’cha hatchi,+ zingwe n’za pakamwa pa bulu,+ ndipo ndodo ndi yokwapulira msana wa anthu opusa.+