Genesis 39:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mkaziyo anali kulankhula ndi Yosefe tsiku ndi tsiku, koma iye sanamvere zoti agone pambali pake, kuti agone naye.+ 1 Mafumu 21:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Palibenso munthu wina wofanana ndi Ahabu.+ Iye anadzipereka kuti achite zoipa pamaso pa Yehova ndiponso mkazi wake Yezebeli+ anamulimbikitsa+ kuchita zimenezo.
10 Mkaziyo anali kulankhula ndi Yosefe tsiku ndi tsiku, koma iye sanamvere zoti agone pambali pake, kuti agone naye.+
25 Palibenso munthu wina wofanana ndi Ahabu.+ Iye anadzipereka kuti achite zoipa pamaso pa Yehova ndiponso mkazi wake Yezebeli+ anamulimbikitsa+ kuchita zimenezo.