Miyambo 26:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Munthu wodana nawe amadzibisa ndi milomo yake, koma mkati mwake mumakhala chinyengo.+ Danieli 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chotero amuna amphamvuwa anati: “Danieliyu sitingamupezere chifukwa chilichonse. Ngati tikufuna kumupezera chifukwa, chikhale chokhudzana ndi lamulo la Mulungu wake.”+ Maliko 7:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Zoipa zonsezi zimatuluka mkatimo ndipo zimaipitsa munthu.”+
5 Chotero amuna amphamvuwa anati: “Danieliyu sitingamupezere chifukwa chilichonse. Ngati tikufuna kumupezera chifukwa, chikhale chokhudzana ndi lamulo la Mulungu wake.”+