Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Miyambo 8:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Pakuti wondipeza ine, ndithu adzapezanso moyo+ ndipo Yehova adzasangalala naye,+

  • Miyambo 16:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Kuzindikira kumakhala ngati chitsime cha moyo kwa ozindikirawo,+ ndipo malangizo* a anthu opusa ndi uchitsiru.+

  • Miyambo 24:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 M’njira yomweyo, dziwa nzeru kuti upindule.+ Ukazipeza, udzakhala ndi tsogolo labwino ndipo chiyembekezo chako sichidzawonongedwa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena