Miyambo 13:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Lamulo la munthu wanzeru ndilo kasupe wa moyo,+ chifukwa limapulumutsa munthu kumisampha ya imfa.+ Miyambo 23:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Chifukwa ukatero udzakhala ndi tsogolo labwino,+ ndipo chiyembekezo chako sichidzawonongedwa.+ Yohane 17:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti moyo wosatha+ adzaupeza akamaphunzira ndi kudziwa+ za inu, Mulungu yekhayo amene ali woona,+ ndi za Yesu Khristu, amene inu munamutuma.+
14 Lamulo la munthu wanzeru ndilo kasupe wa moyo,+ chifukwa limapulumutsa munthu kumisampha ya imfa.+
3 Pakuti moyo wosatha+ adzaupeza akamaphunzira ndi kudziwa+ za inu, Mulungu yekhayo amene ali woona,+ ndi za Yesu Khristu, amene inu munamutuma.+