Miyambo 18:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Dzina la Yehova ndi nsanja yolimba.+ Wolungama amathawira mmenemo ndipo amatetezedwa.+ Yesaya 26:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “Inu anthu anga, pitani mukalowe m’zipinda zanu zamkati ndipo mukatseke zitseko.+ Mukabisale kwa kanthawi mpaka mkwiyo utadutsa.+ Yeremiya 15:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yehova wanena kuti: “Ndithu, ndidzakuchitira zinthu zabwino+ ndipo ndidzakuthandiza kuti ndikupulumutse kwa adani ako pa nthawi ya tsoka+ ndi nthawi ya nsautso.+ Aroma 8:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndiye tinene kuti chiyani pa zinthu zimenezi? Ngati Mulungu ali kumbali yathu, ndani adzatsutsana nafe?+
20 “Inu anthu anga, pitani mukalowe m’zipinda zanu zamkati ndipo mukatseke zitseko.+ Mukabisale kwa kanthawi mpaka mkwiyo utadutsa.+
11 Yehova wanena kuti: “Ndithu, ndidzakuchitira zinthu zabwino+ ndipo ndidzakuthandiza kuti ndikupulumutse kwa adani ako pa nthawi ya tsoka+ ndi nthawi ya nsautso.+
31 Ndiye tinene kuti chiyani pa zinthu zimenezi? Ngati Mulungu ali kumbali yathu, ndani adzatsutsana nafe?+