Genesis 29:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Yakobo anagwira ntchito zaka 7 kuti atenge Rakele.+ Koma iye anangoziona zakazo ngati masiku ochepa chabe, chifukwa anam’konda kwambiri mtsikanayo.+ Miyambo 19:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Cholowa chochokera kwa makolo ndicho nyumba ndi chuma,+ koma mkazi wanzeru amachokera kwa Yehova.+
20 Yakobo anagwira ntchito zaka 7 kuti atenge Rakele.+ Koma iye anangoziona zakazo ngati masiku ochepa chabe, chifukwa anam’konda kwambiri mtsikanayo.+
14 Cholowa chochokera kwa makolo ndicho nyumba ndi chuma,+ koma mkazi wanzeru amachokera kwa Yehova.+