Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 24:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Zichitike kuti, mtsikana amene ndimuuze kuti, ‘Chonde tula pansi mtsuko wako wa madzi kuti ndimweko,’ ndipo amenedi ati andiyankhe kuti, ‘Imwani, ndiponso nditungira madzi ngamila zanu kuti zimwe,’ ameneyo ndi amene mwasankhira mtumiki wanu+ Isaki. Mukachita zimenezo, ndidziwa kuti mwasonyeza mbuyanga chikondi chosatha.”+

  • Genesis 28:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Nyamuka, pita ku Padana-ramu kunyumba ya Betuele bambo a mayi ako. Kumeneko ukatenge mkazi pakati pa ana a Labani mlongo wa mayi ako.+

  • Miyambo 18:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Kodi munthu wapeza mkazi wabwino?+ Ndiye kuti wapeza chinthu chabwino,+ ndipo Yehova amakondwera naye.+

  • Miyambo 31:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Mkazi wabwino, ndani angam’peze?+ Mtengo wake umaposa wa miyala yamtengo wapatali.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena