Rute 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsopano usachite mantha mwana wanga. Ndidzakuchitira zonse zimene wanena,+ chifukwa aliyense mumzinda wathu akudziwa kuti ndiwe mkazi wabwino kwambiri.+ Miyambo 12:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mkazi wabwino ndi chisoti cha ulemu kwa mwamuna wake,*+ koma mkazi wochita zinthu zochititsa manyazi ali ngati chowoletsa mafupa a mwamunayo.+ Miyambo 19:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Cholowa chochokera kwa makolo ndicho nyumba ndi chuma,+ koma mkazi wanzeru amachokera kwa Yehova.+
11 Tsopano usachite mantha mwana wanga. Ndidzakuchitira zonse zimene wanena,+ chifukwa aliyense mumzinda wathu akudziwa kuti ndiwe mkazi wabwino kwambiri.+
4 Mkazi wabwino ndi chisoti cha ulemu kwa mwamuna wake,*+ koma mkazi wochita zinthu zochititsa manyazi ali ngati chowoletsa mafupa a mwamunayo.+
14 Cholowa chochokera kwa makolo ndicho nyumba ndi chuma,+ koma mkazi wanzeru amachokera kwa Yehova.+