Miyambo 18:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kodi munthu wapeza mkazi wabwino?+ Ndiye kuti wapeza chinthu chabwino,+ ndipo Yehova amakondwera naye.+ Miyambo 19:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Cholowa chochokera kwa makolo ndicho nyumba ndi chuma,+ koma mkazi wanzeru amachokera kwa Yehova.+ 1 Akorinto 11:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mwamuna sayenera kuphimba kumutu kwake, popeza iye ndi chifaniziro+ ndi ulemerero+ wa Mulungu, koma mkazi ndi ulemerero wa mwamuna.+
22 Kodi munthu wapeza mkazi wabwino?+ Ndiye kuti wapeza chinthu chabwino,+ ndipo Yehova amakondwera naye.+
14 Cholowa chochokera kwa makolo ndicho nyumba ndi chuma,+ koma mkazi wanzeru amachokera kwa Yehova.+
7 Mwamuna sayenera kuphimba kumutu kwake, popeza iye ndi chifaniziro+ ndi ulemerero+ wa Mulungu, koma mkazi ndi ulemerero wa mwamuna.+