Deuteronomo 34:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako Mose mtumiki wa Yehova+ anafera pamenepo m’dziko la Mowabu, mogwirizana ndi zimene Yehova analamula.+ Yobu 14:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Masiku a munthu ndi odziwika,+Ndipo chiwerengero cha miyezi yake chili ndi inu.Mwamuikira lamulo kuti asalipitirire. Yohane 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inuyo nyamukani mupite ku chikondwereroko. Ine sindipitako panopa, chifukwa nthawi yanga yoyenera+ sinafike.”+
5 Kenako Mose mtumiki wa Yehova+ anafera pamenepo m’dziko la Mowabu, mogwirizana ndi zimene Yehova analamula.+
5 Masiku a munthu ndi odziwika,+Ndipo chiwerengero cha miyezi yake chili ndi inu.Mwamuikira lamulo kuti asalipitirire.
8 Inuyo nyamukani mupite ku chikondwereroko. Ine sindipitako panopa, chifukwa nthawi yanga yoyenera+ sinafike.”+