Salimo 37:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Zinthu zochepa za munthu wolungama ndi zabwino+Kusiyana ndi zinthu zochuluka za anthu ambiri oipa.+ Miyambo 15:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndi bwino kukhala ndi zinthu zochepa ukuopa Yehova,+ kusiyana ndi kukhala ndi zinthu zambiri koma uli ndi nkhawa.+ Miyambo 16:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndi bwino kukhala ndi zinthu zochepa mwachilungamo+ kuposa kukhala ndi zinthu zambiri koma mopanda chilungamo.+ Miyambo 17:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kukhala ndi mkate wouma pali bata,+ kuli bwino kuposa nyumba yodzaza ndi nyama yansembe pali mkangano.+
16 Zinthu zochepa za munthu wolungama ndi zabwino+Kusiyana ndi zinthu zochuluka za anthu ambiri oipa.+
16 Ndi bwino kukhala ndi zinthu zochepa ukuopa Yehova,+ kusiyana ndi kukhala ndi zinthu zambiri koma uli ndi nkhawa.+
8 Ndi bwino kukhala ndi zinthu zochepa mwachilungamo+ kuposa kukhala ndi zinthu zambiri koma mopanda chilungamo.+
17 Kukhala ndi mkate wouma pali bata,+ kuli bwino kuposa nyumba yodzaza ndi nyama yansembe pali mkangano.+