Miyambo 27:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Manda ndiponso malo a chiwonongeko+ sakhuta.+ Nawonso maso a munthu sakhuta.+ Mlaliki 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Munthu wokonda siliva sakhutira ndi siliva, ndipo wokonda chuma sakhutira ndi phindu limene amapeza.+ Zimenezinso n’zachabechabe.+
10 Munthu wokonda siliva sakhutira ndi siliva, ndipo wokonda chuma sakhutira ndi phindu limene amapeza.+ Zimenezinso n’zachabechabe.+