Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mlaliki 4:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Pali munthu amene ali yekhayekha, wopanda mnzake.+ Alibenso mwana kapena m’bale wake,+ koma amangokhalira kugwira ntchito mwakhama. Komanso maso ake sakhutira ndi chuma.+ Iye amafunsa kuti: “Kodi ntchito yovutayi ndikugwirira ndani n’kumadzimana zinthu zabwino?”+ Izinso n’zachabechabe ndiponso ndi ntchito yosautsa mtima.+

  • Mateyu 6:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 “Kapolo sangatumikire ambuye awiri, pakuti adzadana ndi mmodzi ndi kukonda winayo,+ kapena adzakhulupirika kwa mmodzi ndi kunyoza winayo. Simungathe kutumikira Mulungu ndi Chuma nthawi imodzi.+

  • Luka 12:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Kenako anauza anthuwo kuti: “Khalani maso ndipo chenjerani ndi kusirira kwa nsanje kwamtundu uliwonse,+ chifukwa ngakhale munthu atakhala ndi zochuluka chotani, moyo wake suchokera m’zinthu zimene ali nazo.”+

  • 1 Timoteyo 6:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pakuti kukonda+ ndalama ndi muzu+ wa zopweteka za mtundu uliwonse,+ ndipo pokulitsa chikondi chimenechi, ena asocheretsedwa n’kusiya chikhulupiriro ndipo adzibweretsera zopweteka zambiri pathupi lawo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena