Mlaliki 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndaona zinthu zonse m’masiku anga opanda pake.+ Pali munthu wolungama amene amawonongeka akuchita zolungama,+ ndipo pali munthu woipa amene amakhala ndi moyo wautali akuchitabe zoipa.+ Mateyu 27:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pilato anafunsanso kuti: “Nanga Yesu, uja amamuti Khristu, ndichite naye chiyani?” Onse anayankha kuti: “Apachikidwe ameneyo!”+
15 Ndaona zinthu zonse m’masiku anga opanda pake.+ Pali munthu wolungama amene amawonongeka akuchita zolungama,+ ndipo pali munthu woipa amene amakhala ndi moyo wautali akuchitabe zoipa.+
22 Pilato anafunsanso kuti: “Nanga Yesu, uja amamuti Khristu, ndichite naye chiyani?” Onse anayankha kuti: “Apachikidwe ameneyo!”+