Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 4:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Zitatero, Kaini anauza Abele m’bale wake kuti: “Tiye tipite kumunda.” Ali kumeneko, Kaini anam’kantha Abele m’bale wake n’kumupha.+

  • 1 Samueli 22:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Pamapeto pake mfumu inauza Doegi+ kuti: “Iwe, tembenuka ukanthe ansembewa!” Nthawi yomweyo Doegi, Mwedomu,+ anatembenuka n’kukantha ndi kupha+ ansembewo tsiku limenelo, amuna 85 ovala efodi+ wa nsalu.

  • Mateyu 23:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Pa chifukwa chimenechi, tsopano ndikukutumizirani+ aneneri, anthu anzeru ndi aphunzitsi.+ Ena a iwo mudzawapha+ ndi kuwapachika, ndipo ena mudzawakwapula+ m’masunagoge mwanu ndi kuwazunza mumzinda ndi mzinda,

  • Yohane 16:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Anthu adzakuchotsani m’sunagoge.+ Ndipo nthawi ikubwera pamene aliyense wakupha inu adzaganiza kuti wachita utumiki wopatulika kwa Mulungu.+

  • 1 Petulo 4:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Okondedwa, musadabwe ndi moto umene ukuyaka pakati panu, ngati kuti mukukumana ndi chinthu chachilendo. Motowo ukuyaka pofuna kukuyesani.+

  • 1 Petulo 5:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Koma mukavutika kwa kanthawi,+ Mulungu, yemwe amapereka kukoma mtima konse kwakukulu, amenenso anakuitanirani ku ulemerero wake wosatha+ kudzera mu mgwirizano wanu+ ndi Khristu, adzamalizitsa kukuphunzitsani. Adzakulimbitsani+ ndi kukupatsani mphamvu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena