Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Luka 21:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 “Koma zonsezi zisanachitike, anthu adzakugwirani ndi kukuzunzani,+ adzakuperekani kumasunagoge ndi kundende. Adzakutengerani kwa mafumu ndi abwanamkubwa chifukwa cha dzina langa.+

  • Yohane 16:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Anthu adzakuchotsani m’sunagoge.+ Ndipo nthawi ikubwera pamene aliyense wakupha inu adzaganiza kuti wachita utumiki wopatulika kwa Mulungu.+

  • Machitidwe 5:40
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 40 Pamenepo iwo anamvera mawu ake, ndipo anaitanitsa atumwiwo. Ndiyeno anangowakwapula+ ndi kuwalamula kuti asiye kulankhula m’dzina la Yesu,+ kenako anawamasula.

  • 2 Akorinto 11:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Kasanu Ayuda anandikwapula zikoti 40+ kuchotsera chimodzi.

  • 1 Atesalonika 2:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 amene anapha ngakhale Ambuye Yesu+ ndi aneneri+ ndi kuzunzanso ifeyo.+ Ndipo iwo sakukondweretsa Mulungu, koma akutsekereza zinthu zopindulitsa anthu onse.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena