Mlaliki 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Wosonkhanitsa+ anati: “Zachabechabe! Zinthu zonse n’zachabechabe.”+ 2 Timoteyo 2:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chotero, thawa zilakolako zaunyamata,+ koma tsatira chilungamo,+ chikhulupiriro, chikondi, ndi mtendere+ limodzi ndi anthu oitana pa Ambuye ndi mtima woyera.+
22 Chotero, thawa zilakolako zaunyamata,+ koma tsatira chilungamo,+ chikhulupiriro, chikondi, ndi mtendere+ limodzi ndi anthu oitana pa Ambuye ndi mtima woyera.+