Miyambo 15:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Munthu amasangalala ndi yankho lochokera pakamwa pake,+ ndipo mawu onenedwa pa nthawi yoyenera ndi abwino kwambiri.+ Miyambo 16:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Munthu wanzeru mumtima mwake adzatchedwa wozindikira,+ ndipo munthu wolankhula zabwino amakopa ena ndi mawu a pakamwa pake.+ Miyambo 16:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mawu okoma ali ngati chisa cha uchi.+ Amakhala okoma kwa munthu ndipo amachiritsa mafupa.+ Miyambo 25:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mawu olankhulidwa pa nthawi yoyenera ali ngati zipatso za maapozi agolide m’mbale zasiliva.+
23 Munthu amasangalala ndi yankho lochokera pakamwa pake,+ ndipo mawu onenedwa pa nthawi yoyenera ndi abwino kwambiri.+
21 Munthu wanzeru mumtima mwake adzatchedwa wozindikira,+ ndipo munthu wolankhula zabwino amakopa ena ndi mawu a pakamwa pake.+