1 Mafumu 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Solomo anatha zaka 13+ akumanga nyumba yake, ndipo anaimanga n’kuimaliza yonse.+ Mlaliki 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho ndinaona ntchito zonse zimene zinachitidwa padziko lapansi pano,+ ndipo ndinapeza kuti zonse ndi zachabechabe ndiponso zili ngati kuthamangitsa mphepo.+
14 Choncho ndinaona ntchito zonse zimene zinachitidwa padziko lapansi pano,+ ndipo ndinapeza kuti zonse ndi zachabechabe ndiponso zili ngati kuthamangitsa mphepo.+