Salimo 49:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti amaona kuti ngakhale anthu anzeru amafa,+Wopusa ndi wopanda nzeru, onsewo amawonongeka,+Ndipo chuma chawo amasiyira anthu ena.+ Mlaliki 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pakuti munthu wanzeru, mofanana ndi wopusa, sadzakumbukiridwa mpaka kalekale.+ M’masiku amene akubwerawa aliyense adzaiwalidwa. Ndipo kodi wanzeru adzafa motani? Adzafa mofanana ndi wopusa.+
10 Pakuti amaona kuti ngakhale anthu anzeru amafa,+Wopusa ndi wopanda nzeru, onsewo amawonongeka,+Ndipo chuma chawo amasiyira anthu ena.+
16 Pakuti munthu wanzeru, mofanana ndi wopusa, sadzakumbukiridwa mpaka kalekale.+ M’masiku amene akubwerawa aliyense adzaiwalidwa. Ndipo kodi wanzeru adzafa motani? Adzafa mofanana ndi wopusa.+