Miyambo 10:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kwa wopusa, kusonyeza khalidwe lotayirira kuli ngati masewera,+ koma nzeru zimakhala ndi munthu wozindikira.+ Miyambo 23:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Usalankhule m’makutu mwa munthu wopusa,+ chifukwa iye adzanyoza mawu ako anzeru.+
23 Kwa wopusa, kusonyeza khalidwe lotayirira kuli ngati masewera,+ koma nzeru zimakhala ndi munthu wozindikira.+