Nyimbo ya Solomo 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Wachikondi wanga ndi wanga, ndipo ine ndine wake.+ Iye akudyetsera ziweto msipu+ umene uli pakati pa maluwa am’tchire.+ Nyimbo ya Solomo 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Wachikondi wangayo, ine ndine wakewake ndipo iye ndi wangawanga.+ Iye akudyetsera ziweto msipu+ umene uli pakati pa maluwa.”
16 “Wachikondi wanga ndi wanga, ndipo ine ndine wake.+ Iye akudyetsera ziweto msipu+ umene uli pakati pa maluwa am’tchire.+
3 Wachikondi wangayo, ine ndine wakewake ndipo iye ndi wangawanga.+ Iye akudyetsera ziweto msipu+ umene uli pakati pa maluwa.”