Nyimbo ya Solomo 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Wachikondi wangayo, ine ndine wakewake ndipo iye ndi wangawanga.+ Iye akudyetsera ziweto msipu+ umene uli pakati pa maluwa.” Nyimbo ya Solomo 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Wachikondi wangayo, ine ndine wake,+ ndipo iye akulakalaka ineyo.+
3 Wachikondi wangayo, ine ndine wakewake ndipo iye ndi wangawanga.+ Iye akudyetsera ziweto msipu+ umene uli pakati pa maluwa.”