Yohane 15:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Palibe amene ali ndi chikondi chachikulu kuposa cha munthu amene wapereka moyo wake chifukwa cha mabwenzi ake.+ Aroma 16:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iwo anaika miyoyo+ yawo pachiswe chifukwa cha moyo wanga, ndipo si ine ndekha amene ndikuwayamikira,+ komanso mipingo yonse ya anthu a mitundu ina. Aefeso 5:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Amuna inu, pitirizani kukonda akazi anu+ monga mmene Khristu anakondera mpingo n’kudzipereka yekha chifukwa cha mpingowo,+ Chivumbulutso 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iwo anamugonjetsa+ chifukwa cha magazi a Mwanawankhosa,+ ndiponso chifukwa cha mawu a umboni wawo.+ Ndipo iwo sanaone kuti miyoyo yawo ndi yofunika,+ ngakhale pamene anali pa ngozi yoti akhoza kufa.
13 Palibe amene ali ndi chikondi chachikulu kuposa cha munthu amene wapereka moyo wake chifukwa cha mabwenzi ake.+
4 Iwo anaika miyoyo+ yawo pachiswe chifukwa cha moyo wanga, ndipo si ine ndekha amene ndikuwayamikira,+ komanso mipingo yonse ya anthu a mitundu ina.
25 Amuna inu, pitirizani kukonda akazi anu+ monga mmene Khristu anakondera mpingo n’kudzipereka yekha chifukwa cha mpingowo,+
11 Iwo anamugonjetsa+ chifukwa cha magazi a Mwanawankhosa,+ ndiponso chifukwa cha mawu a umboni wawo.+ Ndipo iwo sanaone kuti miyoyo yawo ndi yofunika,+ ngakhale pamene anali pa ngozi yoti akhoza kufa.