Yesaya 18:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pakuti nyengo yokolola isanafike, mitengo ikamaliza kuchita maluwa ndipo mphesa zikamapsa, mlimi amadula mphukira ndi chida chosadzira mitengo ndipo amasadzanso nthambi.+ Yohane 15:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Nthambi iliyonse mwa ine yosabala zipatso amaidula,+ ndipo iliyonse yobala zipatso amaiyeretsa mwa kuitengulira+ kuti ibale zipatso zambiri.+
5 Pakuti nyengo yokolola isanafike, mitengo ikamaliza kuchita maluwa ndipo mphesa zikamapsa, mlimi amadula mphukira ndi chida chosadzira mitengo ndipo amasadzanso nthambi.+
2 Nthambi iliyonse mwa ine yosabala zipatso amaidula,+ ndipo iliyonse yobala zipatso amaiyeretsa mwa kuitengulira+ kuti ibale zipatso zambiri.+